QUR’AN YOLEMEKEZEKA yotanthauzidwa m’chichewa
Share this book QUR’AN YOLEMEKEZEKA yotanthauzidwa m’chichewa Chifukwa chakufunika kwa uthengawu kuti ufike kwa anthu onse, a Bungwe la Africa Muslim Agency adandipempha kuti ndimasulire Qur’an m’chichewa, ndicholinga chakuti amene sangathe kumvetsa uthenga wake m’chiarabu, aumve m’chilankhulo chawo cha Chichewa. Choncho ntchitoyi idagwirikadi kotero kuti munthu akawerenga bwinobwino akhoza kumva uthenga wa Mulungu m’Qur’an. Ndayetsetsa […]
QUR’AN YOLEMEKEZEKA yotanthauzidwa m’chichewa Read More »