Free DownloadNDINGALOWE BWANJI CHISILAMU?
Kodi kulowa chisilamu ndikophweka? ٍ Eya kulowa chisilamu ndikophweka chifukwa sizimasaukila mkhala pakati. Kodi ndikuyenera kuchita changu kulowa chisilamu? kapena ndikuyenera kudikila nthawi yoyenera? kapena ndikuyenera kuthetsa kaye ena mwa mavuto? Ndizoyenera kuchita changu kulowa chisilamu, chifukwa kuchedwetsa kulowa chisilamu kukhoza kubweresa chionongeko, utha kumwalira nthawi iliyonse, ngati mmene zilili kuti kulowa chisilamu ndi Geni(bizinesi…
