Free DownloadMwana wina aliyense amabadwa Mogwirizana ndi chilengedwe (chipembedzo) كل مولود يولد على الفطرة
Mwana wina aliyense amabadwa Mogwirizana ndi chilengedwe (chipembedzo) كل مولود يولد على الفطرة Chichewa التشيشيوا Nkhani ya mwana amene anawerenga mabuku a zipembedzo zosiyanasiyana n’kusankha Chisilamu. Ikusonyeza chikondi chake pa kuphunzira chipembedzo, kuswali, kusala ndi kufunitsitsa kupita ku Makkah. Ndi chikumbutso cha kufunika kophunzitsa ana choonadi ndi kuwasamalira pa chikhulupiliro chawo. Werengani, sinkhasinkhani, ndipo gawanani…

