QUR’AN YOLEMEKEZEKA yotanthauzidwa m’chichewa
QUR’AN YOLEMEKEZEKA yotanthauzidwa m’chichewa Chifukwa chakufunika kwa uthengawu kuti ufike kwa anthu onse, a Bungwe la Africa Muslim Agency adandipempha kuti ndimasulire Qur’an m’chichewa, ndicholinga chakuti amene sangathe kumvetsa uthenga wake m’chiarabu,…


