القرآن الكريم شيشيوا

QUR’AN YOLEMEKEZEKA yotanthauzidwa m’chichewa

QUR’AN YOLEMEKEZEKA yotanthauzidwa m’chichewa

Chifukwa chakufunika kwa uthengawu kuti ufike kwa anthu onse, a Bungwe la Africa Muslim Agency adandipempha kuti ndimasulire Qur’an m’chichewa, ndicholinga chakuti amene sangathe kumvetsa uthenga wake m’chiarabu, aumve m’chilankhulo chawo cha Chichewa. Choncho ntchitoyi idagwirikadi kotero kuti munthu akawerenga bwinobwino akhoza kumva uthenga wa Mulungu m’Qur’an. Ndayetsetsa m’kutanthauzira kwanga mawu oyerawa kuti musakhale zolakwika zambiri, koma ntchito yogwira Munthu siilephera kupezeka zolakwika kupatula zochita za Chauta. Munthu ndi Munthu basi. Choncho ndikupempha aliyense amene angapeze zolakwika pakatanthauzidwe ka Qur’an kapena kasankhidwe kamawu oyerawa, kuti anditumizire ndi cholinga choti pomazatuluka bukuli kachiwiri muzakhale mopanda zolakwika zimenezo.

Pamene ndimagwira ntchitoyi, panali mabuku amene ndimathandizika nawo pakasankhidwe ka kutanthauzira koyenera kwa Qur’an, komanso anthu amene amandithandiza pakasankhidwe ka mawu oyenera m’chichewa. Mabukuwa ndi awa Tafsiri ya Jalalain, Tafsiri ya ibn Kathiri, Al Muntakhab ndi Swafuat Tafaasiri. Ndipo Ntchito yotanthauzira inatha m’chaka cha 1987 pambuyo poigwira mzaka zitatu. Ndipo kuyambira nthawiyo kufikana m’chaka cha 1999 yakhala ikuunikidwa ndi ma Sheikh akuluakulu m’dziko muno.

القرآن الكريم تلغو

దివ్యఖుర్ఆన్ సందేశం

దివ్యఖుర్ఆన్ సందేశం

వివరణ

ఇది తెలుగు భాషలో ఖుర్ఆన్ భావం యొక్క అనువాదము. మొదటి అధ్యాయం నుండి చివరి అధ్యాయం వరకు ఇక్కడ పొందుపరచ బడినది. దీనిని మెరుగుపరచటానికి, మీ సలహాలు ఏమైనా ఉంటే దయచేసి అనువాదకుడికి పంపగలరు. దీని ప్రత్యేకత ఏమిటంటే, ఇందులో ప్రతి అరబీ వచనమునకు దాని ప్రక్కనే తెలుగు అనువాదం చేయబడినది.

WhatsApp Image 2021-08-04 at 2.26.55 PM

Hoe leid ik een gelukkig leven?

السعادة للسعدي

In dit boekje legt Sheikh ’Aboerrahmaan Ibn Naasir al-S’idi uit hoe de mens een gelukkig leven kan leiden en welke middelen hij hiervoor moet toepassen.

WhatsApp Image 2021-08-04 at 12.01.56 PM

پرسش و پاسخ در مورد عادات طبیعی زنان

60 سؤالًا في الحيض للعثيمين

از آنجائيكه جريان و توقف خونهاي طبيعي زنان (حيض و نفاس) در فقه اسلامي تحريم و تحليل بعضي از عبادات و مسائل خانوادگي و زناشوئي از آن ناشي مي شود، اين بود كه مناسب دانستيم بعضي از فتاواي شيخ محمد صالح العثيمين را كه در اين رابطه بصورت سوال و جواب منتشر شده بود انتخاب كرده و آن را در اختيار خواهران مومن قرار دهيم تا شايد قدمي در راه آگاهي آنها در اين رابطه برداشته باشيم.