NDINGALOWE BWANJI CHISILAMU?

Spread the love
Icon
NDINGALOWE BWANJI CHISILAMU?

Kodi kulowa chisilamu
ndikophweka?
ٍ Eya kulowa chisilamu
ndikophweka chifukwa
sizimasaukila mkhala pakati.
Kodi ndikuyenera kuchita
changu kulowa
chisilamu? kapena
ndikuyenera kudikila
nthawi yoyenera? kapena
ndikuyenera kuthetsa
kaye ena mwa mavuto?
Ndizoyenera kuchita changu
kulowa chisilamu, chifukwa
kuchedwetsa kulowa
chisilamu kukhoza
kubweresa chionongeko,
utha kumwalira nthawi
iliyonse, ngati mmene zilili
kuti kulowa chisilamu ndi
Geni(bizinesi yopindula),
choncho nthawi iliyonse
imene munthu akuchita
changu kupita ku geni
phindu lake limakhala
lochuluka.

Kodi kulowa chisilamu
ndikophweka?
ٍ Eya kulowa chisilamu
ndikophweka chifukwa
sizimasaukila mkhala pakati.
Kodi ndikuyenera kuchita
changu kulowa
chisilamu? kapena
ndikuyenera kudikila
nthawi yoyenera? kapena
ndikuyenera kuthetsa
kaye ena mwa mavuto?
Ndizoyenera kuchita changu
kulowa chisilamu, chifukwa
kuchedwetsa kulowa
chisilamu kukhoza
kubweresa chionongeko,
utha kumwalira nthawi
iliyonse, ngati mmene zilili
kuti kulowa chisilamu ndi
Geni(bizinesi yopindula),
choncho nthawi iliyonse
imene munthu akuchita
changu kupita ku geni
phindu lake limakhala
lochuluka.

Shopping Basket