
MITUNDU YA TAUHEED
Kumupatula Allah (olemekezeka) muzinthuzimene wapatulika nazo, kumbali yaumbuye,umulungu ndi maina komanso mbirizake. إفراد الله (عز وجل) بما يختص به من الربوبية, والألوهية, والأسماء والصفات NDIPO MITUNDU YAKE ILIPO ITATU: وأنواعه ثلاثة 1-Tauheed ya umbuye(al-rububiyyah): توحيد الربوبية Kumeneko ndiko kumupatula Allah pa zintchito zake, kapena kumupatula Allah pa kulenga,umwini pa chilichonse ndikuyendetsa zinthu. هو...
MITUNDU YA TAUHEED
Kumupatula Allah (olemekezeka) muzinthuzimene wapatulika nazo, kumbali yaumbuye,umulungu ndi maina komanso mbirizake.
إفراد الله (عز وجل) بما يختص به من الربوبية, والألوهية, والأسماء والصفات
NDIPO MITUNDU YAKE ILIPO ITATU:
وأنواعه ثلاثة
1-Tauheed ya umbuye(al-rububiyyah):
توحيد الربوبية
Kumeneko ndiko kumupatula Allah pa zintchito zake, kapena kumupatula Allah pa kulenga,umwini pa chilichonse ndikuyendetsa zinthu.
هو إفراد الله (عز وجل) بأفعاله أو إفراد الله (عز وجل) بالخلق والملكوالتدبير
2-Tauheed ya umulungu(al-uluhiyyah):
توحيد الألوهية
Uku ndiko kumupatula Allah pompembedza, kapena pa zintchito za akapolo.
هو إفراد الله (عز وجل) بالعبادة أو بأفعال العباد
3- Tauheed ya maina komanso mbiri za Allah(al-Asmãu wa swifat):
توحيد الأسماء والصفات
Uku ndiko kumupatula Allah pa maina omwe wazitchulira yekhakapena mbiri zomwe wazifotokozayekha mu buku lake la Quran, kapena kudzera pa lilime la Mtumiki wake mtendere ndimadalitso zipite kwa iye.
Kumupatulaku kwagona potsindikazomwe iye mwiniwatsindika,ndikuzikana/kuzitsutsazomwe mwini wake azitsutsa,mopanda kusintha kapenakuchotsa mbiri zonse kapena zinamu mbiri za Allah,mopandansokunena kuti mbiri zakezo zilibwanji(mwachitsanzo kunenakuti:ngati wakhala wakhalamotani?), komanso mopandakufanizila ndi mbiri zazolengedwa zake.

MITUNDU YA TAUHEED
Scan QR Code | Use a QR Code Scanner to fast download directly to your mobile device

( وماهو على الغيب بضنين ) viņš nav skops attiecībā uz atklāsmi, nedz arī slinko vēstījuma nodošanā un mācīšanā, bet gan sniedz visas zināšanas, kuras cilvēks ir gatavs saņemt, atšķirībā no zīlniekiem." Zīlnieki neko nedod, nemāca un nesniedz zināšanas, kuras apgalvo zinām, izņemot par samaksu.
April 22, 2025