
SWAUM(KUSALA) ILI MMAGULU AWIRI
SWAUM(KUSALA) ILI MMAGULU AWIRI: الصيام قسمان YOKAKAMIZIKA (WAJIBU): Iyi ndi yomwe imachitika mmwezi wa Ramadhani, ina ndi ya Dipo(kaffarah) ndi ya Lonjezo(nadhir). واجب : في رمضان و الكفارات و النذور YA SUNNAH: Iyi ndi yomwe imachitika posakhala nthawi zitatuzi. نفل : في غير ذلك TANTHAUZO LA SWAUM(KUSALA): تعريف الصيام Uku ndiko kumpembedza Allah posiya kudya, kumwa ndi kena kalikonse komasulisa. Zimenezi kuyambila...
SWAUM(KUSALA) ILI MMAGULU AWIRI
SWAUM(KUSALA) ILI MMAGULU AWIRI: | الصيام قسمان |
YOKAKAMIZIKA (WAJIBU):
Iyi ndi yomwe imachitika mmwezi wa Ramadhani, ina ndi ya Dipo(kaffarah) ndi ya Lonjezo(nadhir). |
واجب : في رمضان و الكفارات و النذور |
YA SUNNAH:
Iyi ndi yomwe imachitika posakhala nthawi zitatuzi. |
نفل : في غير ذلك |
TANTHAUZO LA SWAUM(KUSALA):
|
تعريف الصيام |
Uku ndiko kumpembedza Allah posiya kudya, kumwa ndi kena kalikonse komasulisa.
Zimenezi kuyambila kutuluka kwa fajiri yoona kufikila kulowa kwa dzuwa. |
هو التعبّد لله عز وجل بالإمساك عن الطعام والشراب وسائر المفطّرات من
طلوع الفجر الصادق إلى غروب الشمس. |
SWAUM ILI NDI MSANAMILA ZIWIRI: | للصيام ركنان |
1-CHITSIMIKIZO(NIYAH) | 1 - الــنــيّة |
نيّة الفرض : NIYAH YA KUSALA KWA FARADH | |
Kusala uku zimakakamizika kupanga niyah (Chitsimikizo usiku nthawi ya fajiri iasanakwane.ndipo zimakwanira kupanga niya ya kusalaku kumayambililo kwa mwezi kuti usala mwezi onse wa Ramadhani.Niya malo ake ndi muntima ndipo kuyankhula pa lilime ndi bidia zopeka. | لابدّ من تبييت النيّة في الفرض من الليل - أي:
قبل الفجر - , ويكفي عقد النيّة بدخول الشهر في رمضان , ومحلها القلب , والتلفظ بها بدعة. Kusala uku zimakakamizika kupanga niyah (Chitsimikizo usiku nthawi ya fajiri iasanakwane.ndipo zimakwanira kupanga niya ya kusalaku kumayambililo kwa mwezi kuti usala mwezi onse wa Ramadhani.Niya malo ake ndi muntima ndipo kuyankhula pa lilime ndi bidia zopeka. |
NIYAH YA KUSALA KWA SUNNAH | نيّة النفل NIYAH YA KUSALA KWA SUNNAH : |
Ndi zotheka kupanga niyah nthawi iliyonse dzuwa litatuluka ngati munthu sanapange kalikonse komasulisa swaum (monga kudya), Munthu ameneyu amapeza malipilo akusala kuyambila pamene wapangila niyah. | تصحّ في أي ساعة من النهار
ما لم يأت بمفطّر , ولكن يحسب الأجر من عقد النية. Ndi zotheka kupanga niyah nthawi iliyonse dzuwa litatuluka ngati munthu sanapange kalikonse komasulisa swaum (monga kudya), Munthu ameneyu amapeza malipilo akusala kuyambila pamene wapangila niyah. |
2-Kuzisiya zomasulitsa swaum. | 2- الإمساك
عن المفطرات : 2-Kuzisiya zomasulitsa swaum. |
ZOONONGA SWAUM (KUSALA): | مفسدات الصيام : ZOONONGA SWAUM (KUSALA) |
1-1-kudya kapena kumwa mwadala, choncho amene wadya moiwala swaum yake ndi yabwino bwino. | -1 الأكل أو الشرب عمداَ , فمن نسي فصيامه صحيح:
-kudya kapena kumwa mwadala, choncho amene wadya moiwala swaum yake ndi yabwino bwino. |
2-Kugona ndi mkazi kapena mwamuna:izi zikachitika usana wa mwezi wa Ramadhani,ndipo ochitayo nakhala kuti swaum ndi YOKAKAMIZIKA pa iyeyo, ndiye kuti adzayenera kupeleka dipo lokhwima kwambiri | -2 الجماع , فإذا كان في نهار رمضان والصوم واجب عليه لزمته الكفارة المغلظة
Kugona ndi mkazi kapena mwamuna:izi zikachitika usana wa mwezi wa Ramadhani,ndipo ochitayo nakhala kuti swaum ndi YOKAKAMIZIKA pa iyeyo, ndiye kuti adzayenera kupeleka dipo lokhwima kwambiri. |
3-kutulutsa umuna kapena ukazi. | -3 إنزال المني kutulutsa umuna kapena ukazi. : |
4-Kalikonse kamene kangalowe mu gulu la kudya kapena kumwa, monga jakisoni wa zakudya. | -4 ما كان بمعنى الأكل والشرب , مثل الإبر المغذية:
Kalikonse kamene kangalowe mu gulu la kudya kapena kumwa, monga jakisoni wa zakudya. |
5-Kutulutsa magazi munjira yozichiza (cupping) | -5 إخراج الدم بالحجامة:
Kutulutsa magazi munjira yozichiza (cupping). |
6-kusanza mwadala | -6 التقيؤ عمداّ kusanza mwadala. : |
7-Kutuluka magazi akumwezi( piriodi) kapena aubeleki (nifasi). | -7 خروج دم الحيض و النفاس:
Kutuluka magazi akumwezi( piriodi) kapena aubeleki (nifasi). |
ZINA MWA ZOLOLEDWA KWA OSALA: | بعض ما يباح للصائمZINA MWA ZOLOLEDWA KWA : OSALA |
-Kulawa chakudya.
-Kumeza malovu.
-Kusamba.
-Kutsuka mkamwa ndi mswachi.
-Kuzinunkhiritsa.
-Kuziziziritsa . |
- ذوق الطعام لحاجة Kulawa chakudya. : - بلع الريق: Kumeza malovu . - الاغتسال: Kusamba. - السواك:
Kutsuka mkamwa ndi mswachi. - التطيبKuzinunkhiritsa . : - التبرّد: Kuziziziritsa |
ZOMWE ZIMAPANGITSA KUTI SWAUM IKHALE YOKAKAMIZIKA: | :شروط وجوب الصيام
ZOMWE ZIMAPANGITSA KUTI SWAUM IKHALE YOKAKAMIZIKA |
1-Kukhala Msilamu.
|
1 - الإسـلام
Kukhala Msilamu. |
2-Nzeru. | 2 - الـعـقل
Kukhala ndi nzeru. |
3-Kutha msinkhu.pomwe osatha msinkhu ndiye angolimbikisidwa zosala ndipo omuyang'anira wake azimulamula zakusala | 3 - البلوغ , أما غير البالغ فيرغب في الصيام , ويأمره وليه.
Kutha msinkhu.pomwe osatha msinkhu ndiye angolimbikisidwa zosala ndipo omuyang'anira wake azimulamula zakusala. |
4-Kukhala ndi kuthekela kosala:
Kusala sikukakamizika kwa munthu wa pa ulendo,koma zabwino ndiye kusalako ngati akuona kuti sizimupatsa mavuto.zili choncho chifukwa mtumiki madalitso ndi mtendere zipite kwa iye adayamba wasalako ali pa ulendo. Komanso munthu umamasuka mwachangu,ndipo ndi zopepuka kwa munthu yemwe akulamulidwa zakusala,ndipo amapeza nawo ma ubwino akusala mmwezi wa Ramadhani. |
4 - الاستيطان: فلا يجب الصيام على المسافر , والأولى أن يصوم مالم يشقّ عليه, لفعل
النبي ﷺ ولأنه أسرع في إبراء الذمة وأيسر على المكلف ولإدراك فضيلة الشهر. Kukhala ndi kuthekela kosala: Kusala sikukakamizika kwa munthu wa pa ulendo,koma zabwino ndiye kusalako ngati akuona kuti sizimupatsa mavuto.zili choncho chifukwa mtumiki madalitso ndi mtendere zipite kwa iye adayamba wasalako ali pa ulendo. Komanso munthu umamasuka mwachangu,ndipo ndi zopepuka kwa munthu yemwe akulamulidwa zakusala,ndipo amapeza nawo ma ubwino akusala mmwezi wa Ramadhani. |
5-Kukhala ndi umoyo wa thanzi. | 5 - الـصّـحـة:
Kukhala ndi umoyo wa thanzi. |
6-Kusadwala kumwezi kapena matenda aubeleki
|
6 - الخلو من الحيض والنفاس:
Kusadwala kumwezi kapena matenda aubeleki. |
ZOMWE ZILI ZONYASA KWA MUNTHU OSALA: | مكروهات الصيام :
ZOMWE ZILI ZONYASA KWA MUNTHU OSALA |
1-Kuthila madzi mkamwa ndi mphuno moonjeza. | -1 المبالغة في المضمضة و الاستنشاق:
Kuthila madzi mkamwa ndi mphuno moonjeza. |
2-Kulawa chakudya popanda vuto lililonse | -2 ذوق الطعام لغير حاجة:
Kulawa chakudya popanda chifukwa chilichonse. |
ZIMALETSEDWA KWA MUNTHU OSALA: | يحرم على الصائم :
ZIMALETSEDWA KWA MUNTHU OSALA |
1-Kumeza malovu kapena makhololo koma sizimasulisa swaum | -1 بلع النخامة ولا يفطر بها:
Kumeza makhololo koma sizimasulisa swaum. |
2-Kuphsyophsyonana milomo kwa omwe akuopa kuti atha kuononga swaum yawo. | -2 القبلة لمن لا يأمن فساد صومه:
Kuphsyophsyonana milomo kwa omwe akuopa kuti atha kuononga swaum yawo. |
3-Kutankhula bodza komanso kupanga kalikonse ka haram. | -3 قول الزور (وهو فعل كل محرم):
Kuyankhula bodza komanso kupanga kalikonse ka haram.. |
4-Umbuli | -4 الجهل ( وهو السفاهة):
Umbuli. |
5-Kulumikiza( osamasuka kwa masiku awiri ondondozana usana ndi usiku osadya). | -5 الوصال ( أي ألا يفطر يومين متتاليين):
Kulumikiza( osamasuka kwa masiku awiri ondondozana usana ndi usiku osadya). |
File | |
---|---|
صيام - التشيشيوا .pdf |

SWAUM(KUSALA) ILI MMAGULU AWIRI
Scan QR Code | Use a QR Code Scanner to fast download directly to your mobile device